Pitani ku nkhani yake

Anthu Okwatirana Komanso Mabanja

Baibulo lomwe ndi buku la anthu onse limapereka malangizo omwe angathandize kuti banja lanu likhale losangalala komanso kuti mulere bwino ana anu. a

a Mu chigawo chino, tasintha maina a anthu ena omwe tawagwira mawu.

Kulera Ana

Laibulale

Banja Lanu Likhoza Kukhala Losangalala

Mukhoza kukhala ndi banja losangalala mukamatsatira mfundo za m’Baibulo.