Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Tisaope

Tisaope

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Timakumana ndi zokhoma ndithu.

    Timakhumudwa ndimavutowa.

    Tikasowatu chochita,

    Tisamataye mtima.

    M’lungu

    Alipo.

    (KOLASI)

    Tisaope iye alipo,

    Atithandiza ndi dzanja lakelo.

    Pomwe zinthu zavuta,

    Tisaiwale sitili tokha.

    Tizimupemphatu

    Kuti

    Tisamaope.

  2. 2. Mwatithandiza kupeza ‘nzathu.

    Amatipempherera pomwe zavuta.

    Mawu anu athandiza

    Kuti tizipirirabe

    Mavuto,

    N’zotheka.

    (KOLASI)

    Tisaope iye alipo,

    Atithandiza ndi dzanja lakelo.

    Pomwe zinthu zavuta,

    Tisaiwale sitili tokha.

    Tizimupemphatu

    Ndithu.

    (VESI LOKOMETSERA)

    Tikakumana ndi mavuto,

    Tipirire.

    Zidzayenda.

    (KOLASI)

    Tisaope iye alipo,

    Atithandiza ndi dzanja lakelo.

    Pomwe zinthu zavuta,

    Tisaiwale sitili tokha.

    Tizimupemphatu

    Kuti

    Tisamaope.