Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Ndikukhulupirireni

Ndikukhulupirireni

Pangani Dawunilodi:

  1. 1. Ngati mtengo wodzalidwa,

    Ndi mmene mawuwa

    Achitira mumtimamu, ndapeza mtendere.

    Chiyeso chingabwere,

    Koma ndimakumbuka,

    Nzeru yochoka kumwamba yandithandiza

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Kuti ndisaope.

    Ndiyembekeze Yehova.

    (KOLASI)

    Mavuto ndapirira,

    Ndalimba ndi mawuwa.

    Tsiku ndi tsiku ndikhulupirire inu.

  2. 2. Mayesero akhoza

    Kundifooketsadi,

    Ndimakumbukira kuti muli nane

    Ndikamaganizira​—

    Ndimasunga mawuwa

    Mumtima kuti anditsogoleredi—

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Kuti ndisaope.

    Ndiyembekeze Yehova.

    Mavuto, ndipirire ndithu.

    Ndiziganizira za mphoto.

    (KOLASI)

    Mavuto ndapirira,

    Ndalimba ndi mawuwa.

    Tsiku ndi tsiku ndikhulupirire inu​—

    Inu.

    (KUKONZEKERA KOLASI)

    Kuti ndisaope.

    Ndiyembekeze Yehova.

    Mavuto, ndipirire ndithu.

    Ndiziganizira za mphoto.

    (KOLASI)

    Mavuto ndapirira,

    Ndalimba ndi mawuwa.

    Tsiku ndi tsiku ndikhulupirire inu.