Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

JW LANGUAGE

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Okhudza JW Language (Pa Zipangizo za Windows)

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri Okhudza JW Language (Pa Zipangizo za Windows)

Pulogalamu Yophunzirira Chinenero ya pa JW imagwira ntchito pa zipangizo izi:

  • Mafoni, Matabuleti komanso makompyuta a Windows 8.1

Zinthu zina zomwe zingakuthandizeni kugwiritsa ntchito pulogalamu imeneyi ziyamba kupezeka posachedwapa:

Panopa tilibe maganizo odzakhala ndi zinthu zothandiza pogwiritsa ntchito zipangizo zotsatirazi:

  • Makompyuta a Windows 7 komanso ena a m’mbuyomu

  • Mafoni a Windows 8.0 komanso ena a m’mbuyomu

 

Munthu wina amene amadziwa bwino kugwiritsa ntchito Pulogalamu Yophunzirira Chinenero ya pa JW akhoza kukuthandizani. Ngati palibe, lembani fomu yokuthandizani kupeza mayankho ndipo kenako tumizani fomuyo.