Ntchito Yathu Yolalikira

NTCHITO YOLALIKIRA

Ntchito Yolalikira Mwapadera Inayenda Bwino ku Lapland

Onani zimene anthu a ku Lapland anachita pa ntchito yapadera imene a Mboni anagwira pofuna kuwathandiza.

NTCHITO YOLALIKIRA

Ntchito Yolalikira Mwapadera Inayenda Bwino ku Lapland

Onani zimene anthu a ku Lapland anachita pa ntchito yapadera imene a Mboni anagwira pofuna kuwathandiza.

“Mphatso Yochokera kwa Mulungu” Pachionetsero cha ku Treasure City

Aphunzitsi ndi ana a sukulu anasangalala kwambiri ndi Mabaibulo, mabuku ndi mavidiyo omwe anali kuchionetsero cha mabuku ku Gaudeamus m’dziko la Romania.

Kulalikira kwa Anthu a Mtundu wa Sinti ndi Roma ku Germany

Mu 2016, a Mboni anagwira ntchito yapadera yokalalikira anthu a mtundu wa Sinti ndi Roma ndipo anagawira timapepala pafupifupi 3,000 komanso anayamba maphunziro a Baibulo 19.

Kuchita Ulaliki wa Mashelefu Amatayala M’malo Amene Anthu Amakachitira Holide ku Germany

A Mboni za Yehova anaika timashelefu ku Berlin, Cologne, Hamburg, Munich, ndi m’mizinda ina. Kodi timashelefuti tikuthandizadi anthu a ku Germany tikaikidwa m’madera amene amakapangirako maholide?

Pachionetsero cha ku Botswana Panali Chuma Chamtengo Wapatali

Ana omwe anafika pamalowa anachita chidwi kwambiri ndi mavidiyo a makatuni a mutu wakuti Khalani Bwenzi la Yehova omwe amathandiza anthu kugwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo.

Kulalikira Uthenga Wabwino kwa Ogwira Ntchito musitima

Pofuna kuthandiza ogwira ntchito musitima omwe akhalira kuyenda, a Mboni akhazikitsa pulogalamu yophunzitsa Baibulo ndi anthuwa madoko akuluakulu. Kodi ogwira ntchito musitimawa amawalandira bwanji a Mboniwo?

Kulalikira Mumzinda wa Paris

A Mboni za Yehova anagwira ntchito yodziwitsa anthu za nthawi imene anthu sadzawononganso chilengedwe padzikoli.

A Mboni za Yehova Akulalikira M’madera Akutali Kwambiri

A Mboni za Yehova amachita khama kuphunzitsa anthu Baibulo kumadera akutali kwambiri ngakhale kuti amakumana ndi mavuto ochuluka.

Akulalikira Anthu Amitundu Yosiyanasiyana ku Canada

A Mboni za Yehova amalalikira m’zilankhulo zosiyanasiyana n’cholinga choti anthu aphunzire za Mlengi wathu m’chilankhulo chawo.

Anthu Oyambirira Kukhala ku America Anachita Chikondwerero ku New York

Pachikondwerero cha ku New York mu 2015, anthu ambiri anachita chidwi ndi mabuku amene a Mboni za Yehova anabweretsa omwe anali m’zilankhulo za anthu oyambirira kukhala ku America.

Amadutsa Pamchenga wa Pansi pa Nyanja Kupita Kokalalikira

A Mboni za Yehova anapeza njira yowathandiza kuti azikalalikira anthu a patizilumba ta Halligen.

Chiwerengero cha Mboni za Yehova Chakwera Kwambiri

Pofika mu August 2014, padziko lonse panali a Mboni za Yehova oposa 8 miliyoni. Kodi chiwerengero chawo chakwera bwanji kuchokera pambuyo pa nkhondo yoyamba ya padziko lonse?

Ku France Kunachitika Chionetsero Chapadera cha Baibulo

Anthu amene anapita kuchionetsero cha zinthu za m’mayiko osiyanasiyana cha 2014 chomwe chinali mumzinda wa Rouen ku France anachita chidwi kwambiri ndi malo ena omwe analembapo kuti ‘Baibulo ndi Lothandiza Kuyambira Kale, Panopa Komanso M’tsogolo.’

Webusaiti ya JW.ORG Ikuthandiza Anthu Kumva Uthenga wa M’Baibulo

A Mboni za Yehova, ana ndi akulu omwe, akusangalala kugwiritsa ntchito webusaiti yawo yomwe ndi yosavuta kugwiritsa ntchito pouza anthu ambirimbiri uthenga wabwino wa Ufumu wa Mulungu.

Kulalikira M’dera Lakutali​—Australia

Onerani vidiyo yosonyeza banja lina la Mboni za Yehova likulalikira uthenga wa m’Baibulo kwa anthu a kudera lakutali m’dziko la Australia.

Kulalikira M’mbali mwa Mtsinje wa Xingu

Gulu la a Mboni za Yehova okwana 28, linagwiritsa ntchito boti lotalika mamita 15 n’cholinga chokalalikira za Ufumu wa Mulungu, kwa anthu a m’midzi ya m’mbali mwa mtsinje wa Xingu.

Anthu Okonda Mtendere Anasonkhana pa Mwambo wa Armada

A Mboni za Yehova anagwiritsa ntchito matebulo a matayala popereka mabuku kwa ulele kwa anthu amene anabwera ku mwambo umene unachitikira ku France.

Kulalikira M’dera Lakutali M’dziko la Ireland

Banja likufotokoza mmene ntchito yolalikira ku Ireland, yawathandizira kukhala ogwirizana.

Sukulu ya Giliyadi Yakwanitsa Zaka 70

Pa February 1, 1943, kalasi yoyamba ya sukulu yapadera kwambiri inayamba m’dera la kumpoto ku New York. Sukuluyi yathandiza anthu masauzande ambiri kuti azigwira ntchito yolalikira komanso kuphunzitsa ena za Mulungu.

Anzanutu Akuphunzira Chibengali

N’chifukwa chiyani anthu 23 a Mboni za Yehova ku Queens m’chigawo cha New York, ku U.S.A., ayamba kuphunzira Chibengali?

A Mboni za Yehova Akugwira Ntchito Yatsopano ku Manhattan, New York

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe ntchito yapadera imene tikugwira pofuna kuthandiza anthu kudziwa uthenga wa m’Baibulo.