Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo

ANA AZAKA ZOSAPITIRIRA ZITATU

Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo

Ona nyama zimene zili pafupi ndi chingalawa cha Nowa.

Kodi ndi nyama ziti zimene zimalira ngati ng’ombe? Nanga ndi ziti zimene zimauwa?

Chingalawa cha Nowa chinapulumutsa nyama zonse, zazifupi ndi zazitali. Genesis 7:7-10; 8:15-17

ZOTI MAKOLO ACHITE

Muuzeni mwana wanuyo kuti aloze:

Chingalawa

Chimbalangondo

Galu

Njovu

Kadyamsonga

Mkango

Nyani

Nkhumba

Nkhosa

Mbidzi

Utawaleza

Mtengo

Kodi ungathe kuyerekeza mmene nyama izi zimalirira?

Galu

Mkango

Nyani

Nkhumba

Nkhosa