Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NSANJA YA OLONDA Na. 2 2021 | Dziko Labwino Lili Pafupi

Kodi zinthu zimene zikuchitika padzikoli zikusonyeza kuti dziko latsala pang’ono kutha? Ngati ndi choncho tingatani kuti tidzapulumuke mapeto a dzikoli? Nanga chidzachitike n’chiyani dzikoli likadzatha? Nkhani za m’magaziniyi zitithandiza kudziwa mayankho otonthoza ochokera m’Baibulo a mafunso amenewa.

 

Tikufunikira Dziko Labwino

Zinthu zimene zikuchitika padzikoli zikusonyeza kuti tikufunikira dziko labwino.

Kodi Dzikoli Lidzatha?

Baibulo limanena zokhudza mapeto a dzikoli koma limanenanso kuti anthu adzakhala padzikoli mpaka kalekale.

Kodi Mapeto Adzafika Liti? Zimene Yesu Ananena

Kodi zinthu zimene Yesu ananena kuti zidzachitika mukuziona?

Kodi Mungatani Kuti Mudzakhale M’dziko Latsopano?

Kodi kukhala pa ubwenzi wolimba ndi Mulungu kungathandize bwanji munthu kuti adzapulumuke?

Dziko Latsopano Lili Pafupi

Kodi zinthu zidzakhala bwanji padzikoli Mulungu akadzakwaniritsa malonjezo ake onse?

Kodi Dzikoli Latsala Pang’ono Kutha?

Mungadabwe kumva zimene Baibulo limanena.