Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

“Mtima Wodekha Ndiwo Moyo wa Munthu”

“Mtima Wodekha Ndiwo Moyo wa Munthu”

Mawu amenewa omwe amapezeka pa Miyambo 14:30, analembedwa pafupifupi zaka 3,000 zapitazo. Mawuwa amasonyeza kuti mfundo za m’Baibulo n’zothandiza nthawi zonse. Ngati mukufuna kudziwa zambiri, pitani pawebusaiti yathu ya jw.org. Pawebusaitiyi mungapezepo mavidiyo, makatuni, zochitika pamoyo wa anthu ena komanso nkhani zambiri zomwe zingakuthandizeni kuchepetsa nkhawa. Mungapezepo nkhani zokhudza: