Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Zosangalatsa

Zosangalatsa

Chigawo 8

Zosangalatsa

Kodi mumachita kangati zinthu zosangalatsa, monga kuchita masewera olimbitsa thupi, kumvera nyimbo, kuonera TV ndi kuchita masewera a pakompyuta?

□ Mwa apo ndi apo

□ Kamodzi patsiku

□ Kangapo patsiku

Kodi ndani amakuchititsani kusankha zosangalatsa zimene mumakonda?

□ Anzanu

□ Makolo anu

□ Oitanira malonda

Masiku ano kuli zosangalatsa zambiri zimene achinyamatanu mungasangalale nazo. Koma nthawi imene muli nayo ndi yochepa. Ndipo zosangalatsa zimene mungasankhe zingakhudze khalidwe lanu komanso mmene mumaganizira. Choncho, kodi mungasankhe bwanji zosangalatsa zoyenera? Ndipo kodi muyenera kuzichita nthawi yochuluka bwanji? Mitu 30 mpaka 33 ikuthandizani kudziwa mmene mungasankhire zosangalatsa zabwino.

[Chithunzi chachikulu pamasamba 244, 245]