Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Kukula Mwauzimu

Kukula Mwauzimu

Chigawo 9

Kukula Mwauzimu

Pazinthu zotsatirazi, kodi ndi chiti chimene chimakuvutani kwambiri?

□ Kuphunzira Baibulo

□ Kupemphera nthawi zonse kwa Yehova Mulungu

□ Kufotokozera ena (makamaka achinyamata anzanga) za chikhulupiriro changa

□ Kumvetsa kufunika kotsatira mfundo za m’Baibulo

Pamzere uli m’munsiwu, lembani zimene mukufuna kuchita kuti muthetse vuto lanulo.

․․․․․

Werengani Mitu 34 mpaka 38 kuti muone zimene mungachite kuti muzitsatira mfundo za m’Baibulo pa moyo wanu, ubwenzi wanu ndi Mulungu ukhale wolimba ndiponso kuti mukhale ndi zolinga zokuthandizani kukhala ndi moyo watanthauzo.

[Chithunzi chachikulu pamasamba 280, 281]