Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

March 20-26

2 MBIRI 1-4

March 20-26

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI

  • Kuitanira Anthu ku Chikumbutso: (3 min.) Itanirani mnzanu wakuntchito, wakusukulu kapena wachibale wanu. (th phunziro 2)

  • Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pangani ulendo wobwereza kwa munthu amene anasonyeza chidwi ndipo analandira kapepala komuitanira ku Chikumbutso. Mufotokozereni zokhudza phunziro la Baibulo la ulele, kenako mugawireni kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?, kenako kambiranani naye mfundo za muvidiyoyi. (th phunziro 17)

  • Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 09 mfundo 5 (th phunziro 9)

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

  • Nyimbo Na. 19

  • Kodi Mwalikonzekera Tsiku Lofunika Kwambiri la Pachaka?: (15 min.) Nkhani komanso vidiyo. Ikambidwe ndi woyang’anira utumiki. Fotokozani mmene ntchito yoitanira anthu ku Chikumbutso ikuyendera. Funsani mafunso anthu amene akumana ndi zosangalatsa. Tchulani za ndandanda yowerengera Baibulo pa nyengo ya Chikumbutso yomwe ili pa tsamba 8 ndi 9, ndipo limbikitsani onse kuti akonzekeretse mitima yawo. (Eza 7:10) Kambiranani zimene tingachite kuti tidzalandire bwino alendo athu pa Tsiku la Chikumbutso. (Aro 15:7; mwb16.03 2) Onerani vidiyo yakuti, Mmene Mungapangire Mkate wa Chikumbutso.

  • Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 41 mfundo 1-4

  • Mawu Omaliza (3 min.)

  • Nyimbo Na. 135 ndi Pemphero