Onani zimene zilipo

Kugwilitsila Nchito Webusaiti ya JW.ORG Polalikila Uthenga wa m’Baibulo

Kugwilitsila Nchito Webusaiti ya JW.ORG Polalikila Uthenga wa m’Baibulo

Pa August 27, 2012, Mboni za Yehova zinayamba kugwilitsila nchito webusaiti yokonzedwanso ya jw.org. Onani mmene Mboni za Yehova ndi anthu ena apindulila ndi webusaitiyi..