Mafunso Amene Amafunsidwa Kawili-kaŵili Ponena za Mboni za Yehova

Kodi a Mboni za Yehova amalalikila nyumba na nyumba kuti akapulumuke?

Dziŵani zimene timakhulupilila za cipulumutso, komanso mmene timacilandilila.

Kodi a Mboni za Yehova amalalikila nyumba na nyumba kuti akapulumuke?

Dziŵani zimene timakhulupilila za cipulumutso, komanso mmene timacilandilila.

Kodi Bungwe Lolamulila la Mboni za Yehova N’ciyani?

Kodi a m’bungweli ndiwo atsogoleli a gulu lathu?

Kodi Mboni za Yehova Zimakhulupilila Yesu?

Dziŵani cifukwa cake Akristu oona afunika kukhulupilila Yesu.

Kodi Mboni za Yehova Zimakhulupilila Kuti Cipembedzo Cao Ndico Cokha Coona?

Kodi Yesu anakamba kuti pali njila zambili zimene zimatsogolela ku cipulumutso?

Kodi Mboni za Yehova Zimakhulupilila Kuti Ndizo Zokha Zidzapulumuka?

Baibulo limafotokoza amene adzakhala ndi mwai wopulumuka.

Kodi Mboni za Yehova Zimalemekeza Zipembedzo Zina?

Dziŵani mmene kulemekeza zipembedzo zina kumadziŵikitsila Akristu oona.

N’cifukwa ciani Timachedwa Mboni za Yehova?

Ŵelengani kuti mudziŵe kumene dzina lathu linacokela.

Ndani Anayambitsa Cipembedzo ca Mboni za Yehova?

Ŵelengani kuti mudziŵe, kuti Charles Taze Russell sindiye anayambitsa cipembedzo ca Mboni za Yehova.

Kodi Ndalama Zoyendetsela Nchito ya Mboni za Yehova Zimacokela Kuti?

Ŵelengani kuti mudziŵe cifukwa cake nchito yolalikila padziko lonse ikupita patsogolo kwambili ngakhale kuti sitiyendetsa mbale ya zopeleka ndi kupeleka cakhumi.

Kodi Mboni za Yehova Zili ndi Abusa Amene Amalipilidwa?

Kodi muli ndi anthu amene amaonedwa kuti ndi apadela? Ndani amagwila nchito yolalikila?

Kodi Mipingo Yanu Imayendetsedwa Bwanji?

Dziŵani mmene timalandilila citsogozo ndi malangizo mumpingo.

Kodi Bungwe Lolamulila la Mboni za Yehova N’ciyani?

Kodi a m’bungweli ndiwo atsogoleli a gulu lathu?

Kodi Bungwe la Watch Tower Bible and Tract Society N’ciani?

Kodi a Mboni za Yehova amaseŵenzetsa bwanji bungweli?

N’cifukwa Ciani Mboni za Yehova Zimalalikila Kunyumba ndi Nyumba?

Normal;Onani zimene Yesu anauza ophunzila ake oyambilila kuti azicita.

Kodi a Mboni za Yehova amalalikila nyumba na nyumba kuti akapulumuke?

Dziŵani zimene timakhulupilila za cipulumutso, komanso mmene timacilandilila.

N’cifukwa Ciani Mboni za Yehova Zimalalikila Anthu Amene Ali Kale ndi Cipembedzo Cao?

N’ciani cimatilimbikitsa kulalikila anthu amene ali kale ndi cipembedzo cao?

Kodi Phunzilo la Baibulo N’ciani?

Pezani mayankho a mafunso okhudza mmene timacitila phunzilo la Baibulo laulele.

Kodi a Mboni za Yehova Ali na Baibo Yawo-yawo?

Kugwilitsa nchito ma Baibo azimasulilo zosiyana-siyana kungakupindulileni kwambili pophunzila Baibo. Pali mfundo zitatu zapadela zokhudza Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika zimene zingakupangitseni kufuna kuiphunzila

N’cifukwa Ciani Mboni za Yehova Sizikondwelela Khrisimasi?

Anthu ambili amakondwelela Khrisimasi ngakhale kuti amadziŵa ciyambi cake. Dziŵani cifukwa cake Mboni za Yehova sizikondwelela Khrisimasi.

Kodi Mboni za Yehova ndi Akristu?

Dziŵani zimene zimatisiyanitsa ndi zipembedzo zina zimene zimati n’zacikristu.

Kodi Mboni za Yehova ndi Gulu Lampatuko la ku America?

Mfundo zinai zimene muyenela kudziŵa zokhudza gulu la padziko lonse la Mboni za Yehova.

Kodi a Mboni za Yehova Amapewa Anthu Amene Kale Anali M’cipembedzo Cao?

Kucotsa munthu mumpingo ndi koyenela ndipo kungathandize munthuyo kokonzanso ubwenzi wake ndi Mulungu.