Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

JW LIBRARY SIGN LANGUAGE

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri—JW Library Sign Language

Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri—JW Library Sign Language

JW Library Sign Language imagwira pa zipangizo izi:

  • Matabuleti ndi mafoni a Android Version 5.1 kapena yaposachedwapa

  • iPad 4 kapena ina yatsopano (ya iOS 10.0 kapena yaposachedwapa)

  • iOS 12.0 kapena yaposachedwapa)

  • Matabuleti, makompyuta ndi mafoni a Windows 10 (Version 1903 kapena yaposachedwapa)

 

Mukapanga dawunilodi buku, JW Library Sign Language imapanga dawunilodi tsamba lokhala ndi Mitu ya Nkhani kuphatikizapo mitu ya nkhanizo ndiponso zithunzi.

Dinani batani lakuti Pangani Dawunilodi lomwe lili pamwamba kuti mupange dawunilodi mavidiyo onse okhudza bukulo, kapena dinani batani la Pangani Dawunilodi lomwe lili pafupi ndi vidiyo imene mukufuna kupanga dawunilodi.

Mnzanu amene amadziwa kagwiritsidwe ntchito ka JW Library Sign Language akhoza kukuthandizani. Ngati sangathe, chonde lankhulani ndi a ku ofesi ya nthambi yomwe muli nayo pafupi.