Pitani ku nkhani yake

Nyimbo 120—Khalani Omvera Kuti Mulandire Madalitso

Nyimbo 120—Khalani Omvera Kuti Mulandire Madalitso

Tikhoza kukhala bwenzi la Yehova poimba nyimbo. Tiyeni tiimbe nyimbo limodzi ndi Kalebe ndi Sofiya. Nyimboyi ikunena za madalitso omwe tingapeze chifukwa chomvera Yehova.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

MAVIDIYO

Phunzirani kwa Anzake a Yehova

Phunzirani zambiri kuchokera kwa anthu otchulidwa m’Baibulo omwe anakhala mabwenzi a Yehova!

ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA

Zoti Ana Achite

Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.