ZOTI MUCHITE Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muzipewa Kuonera Zolaula YAMBANI Zimene zingakuthandizeni kukana mayesero. Koperani Nkhani Zina Zoti Achinyamata Achite Achinyamata Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kupewa Kuonerera Zolaula? Kodi kuonera zolaula n’kofanana motani ndi kusuta fodya? ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Mukulephera Kusiya Kuonerera Zinthu Zolaula? Baibulo lingakuthandizeni kuti mumvetse cholinga cha zinthu zolaula. ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA Kodi Ndiyenera Kudziwa Zotani pa Nkhani Yotumizirana Mameseji ndi Zinthu Zina Zolaula? Kodi munthu wina amakukakamizani kuti mumutumizire zolaula? Kodi kutumizirana zolaula kuli ndi mavuto otani? Kodi ndi kukopana basi? GALAMUKANI! Mungatani Kuti Musamagonje Mukakumana ndi Mayesero? Mwamuna komanso mkazi weniweni amatha kupewa mayesero. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zinthu 6 zimene zingakuthandizeni kusagonja mukamayesedwa komanso kuti musakhale ndi nkhawa chifukwa chodziwa kuti mwagonja. Mfundo Zofunika za M'Baibulo—Mavidiyo Kodi Kuonera Zolaula Ndi Tchimo? Kodi mawu akuti “zolaula” amapezeka m’Baibulo? Kodi tingadziwe bwanji mmene Mulungu amaonera nkhani yoonera zolaula? Patsani ena Patsani ena Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muzipewa Kuonera Zolaula ZOTI ACHINYAMATA ACHITE Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muzipewa Kuonera Zolaula Chichewa Zimene Zingakuthandizeni Kuti Muzipewa Kuonera Zolaula https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502014197/univ/art/502014197_univ_sqr_xl.jpg