Mboni za Yehova Padziko Lonse

Virgin Islands, U.S.

Mfundo Zachidule—Virgin Islands, U.S.

  • 104,000—Chiwerengero cha anthu
  • 536—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 8—Mipingo
  • Pa anthu 205 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho

Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.