Mboni za Yehova Padziko Lonse

Philippines

  • Manila, Philippines​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo m’boma la Intramuros

  • Philippines—Akuitanira anthu kumisonkhano ya mpingo m’dera la Baler m’chigawo cha Aurora

  • Manila, Philippines​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo m’boma la Intramuros

  • Philippines—Akuitanira anthu kumisonkhano ya mpingo m’dera la Baler m’chigawo cha Aurora

Mfundo Zachidule—Philippines

  • 113,964,000—Chiwerengero cha anthu
  • 253,876—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 3,552—Mipingo
  • Pa anthu 464 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Ndayesetsa Kukhala “Zinthu Zonse kwa Anthu Osiyanasiyana”

Utumiki wosiyanasiyana umene Denton Hopkinson anachita unamuthandiza kuona kuti Yehova amakonda anthu a mitundu yonse.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Philippines

Onani zimene zinalimbikitsa anthu ena kuti asiye ntchito yawo komanso kugulitsa katundu wawo n’kukakhala kumadera akumidzi ku Philippines.