Mboni za Yehova Padziko Lonse

Kenya

Mfundo Zachidule—Kenya

  • 55,101,000—Chiwerengero cha anthu
  • 31,017—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 605—Mipingo
  • Pa anthu 1,863 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Yehova Wandidalitsa Kuposa Mmene Ndinkaganizira

Kuchita umishonale ku Africa kunathandiza Manfred Tonak kuti akhale ndi makhalidwe abwino ambiri monga kuleza mtima komanso moyo wosalira zambiri.