Mboni za Yehova Padziko Lonse

Greece

  • Monastiraki Square, Athens, Greece—Akugawira magazini ya Galamukani!

Mfundo Zachidule—Greece

  • 10,482,000—Chiwerengero cha anthu
  • 27,759—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 345—Mipingo
  • Pa anthu 379 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

Nkhondo Yomenyera Ufulu Wolalikira Yomwe Inatenga Zaka 50

Mu 1993, a Minos Kokkinakis anapambana pa nkhondo yazaka 50 yomenyera ufulu wopembedza. Aka kanali koyamba kuti Khoti Loona za Ufulu wa Anthu ku Europe ligamule kuti dziko laphwanyira anthu ufulu wopembedza.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Ndine Msilikali wa Khristu

Demetrius Psarras anamangidwa chifukwa chokana kulowa usilikali. Komabe anapitiriza kuthandiza kuti Mulungu atamandike ngakhale atakumana ndi mayesero oopsa.