Mboni za Yehova Padziko Lonse

Antigua and Barbuda

Mfundo Zachidule—Antigua and Barbuda

  • 100,000—Chiwerengero cha anthu
  • 481—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 7—Mipingo
  • Pa anthu 216 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

NKHANI

A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho

Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.