Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

NYIMBO 157

Kudzakhala Mtendere

Kudzakhala Mtendere

(Salimo 29:11)

  1. 1. Pomwe dziko likusowa

    mtendere

    Ife tili ndi mtendere.

    Sitida nkhawa

    Chifukwa Yehova

    Adzathetsatu

    mavuto.

    (KOLASI)

    Padziko lapansi

    Padzakhalatu

    Mtendere wosatha.

    Mavuto akatha,

    Tidzapumula.

    Konse kudzakhala

    Mtendere.

  2. 2. Tikalowa m’dziko

    Latsopano

    Moyo udzasangalatsa.

    Mtendere womwe

    Tikulakalaka

    Yehova adzatipatsa.

    (KOLASI)

    Padziko lapansi

    Padzakhalatu

    Mtendere wosatha.

    Mavuto akatha,

    Tidzapumula.

    Konse kudzakhala

    Mtendere.

    (KOLASI)

    Padziko lapansi

    Padzakhalatu

    Mtendere wosatha.

    Mavuto akatha,

    Tidzapumula.

    Tidzasangalala!

    (KOLASI)

    Padziko lapansi

    Padzakhalatu

    Mtendere wosatha.

    Mavuto akatha,

    Tidzapumula.

    Konse kudzakhala

    Mtendere,

    Mtendere!