Pitani ku nkhani yake

Zimene Achinyamata Amafunsa—Kodi Ndingapeze Bwanji Anzanga Abwino?

Achinyamata ambiri amaona kuti kupeza anzawo ocheza nawo n’kovuta. Onani zimene Tara anachita kuti apeze anzake abwino omwenso amamukonda. Kenako muganizire zimene inunso mungachite kuti mupeze anzanu abwino. Muonanso zimene achinyamata a m’mayiko osiyanasiyana anachita kuti apeze anzawo abwino.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ACHINYAMATA

Zimene Achinyamata Amafunsa, Buku Lachiwiri

Zina mwa nkhani zimene mungawerenge ndi zokhudza sukulu, zosangalatsa, anzathu, makolo, kusintha kwa thupi, mtima wanu komanso anyamata kapena atsikana.

MAVIDIYO AMAKATUNI

Kodi Mnzako Weniweni Ungamudziwe Bwanji?

N’zosavuta kupeza anzanu amene sangakuthandizeni, koma kodi mungapeze bwanji mnzanu weniweni?