Pitani ku nkhani yake

Pitani ku mitu ya nkhani

Zinthu Padzikoli Zinasintha Kuyambira mu 1914

Zinthu Padzikoli Zinasintha Kuyambira mu 1914

Baibulo limafotokoza zinthu monga makhalidwe ndi zochitika zomwe zingatithandize kudziwa kuti tili “m’masiku otsiriza.” (2 Timoteyo 3:1) Onani kuti zizindikirozi zakhala zikuonekera kuposa kale lonse kuyambira m’chaka cha 1914.