NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) June 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira August 12–​September 8, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 23

Yehova Akutiitana Kuti Tikhale Alendo Ake

Idzaphunziridwa mlungu wa August 12-18, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 24

Pitirizani Kukhala Alendo a Yehova Mpaka Kalekale

Idzaphunziridwa mlungu woyambira August 19-25, 2024.

MBIRI YA MOYO WANGA

Yehova Wakhala Akuyankha Mapemphero Anga

Kodi n’chiyani chomwe chinatsimikizira Marcel Gillet yemwe anali wachikulire kuti Yehova ndi “Wakumva pemphero”?

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi mawu akuti “Mudzawayang’anira” opezeka pa Salimo 12:7, akunena za “ovutika” (vesi 5) kapena “mawu a Yehova” (vesi 6)?

NKHANI YOPHUNZIRA 25

Muzikumbukira Yehova Yemwe ndi “Mulungu Wamoyo”

Idzaphunziridwa mlungu wa August 26–​September 1, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 26

Muzidalira Yehova Yemwe ndi Thanthwe Lanu

Idzaphunziridwa mlungu wa September 2-8, 2024.