Pulogalamu ya Msonkhano wa 2021

Lachisanu

Pulogalamu ya Lachisanu yachokera pa Luka 17:5​—“Tiwonjezereni chikhulupiriro.”

Loweruka

Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Yuda 3​—‘Menya mwamphamvu nkhondo yachikhulupiriro.’

Lamlungu

Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Mateyu 21:21​—“Ngati mutakhala ndi chikhulupiriro . . . , zidzachitikadi.”

Mawu kwa Osonkhana

Mawu othandiza anthu amene abwera pamsonkhano.