Onani zimene zilipo

APRIL 17, 2023
NKHANI ZA PADZIKO LONSE

Ciunikilo Na. 3 ca Bungwe Lolamulila mu 2023

Ciunikilo Na. 3 ca Bungwe Lolamulila mu 2023

Mu lipoti lino, wa m’Bungwe Lolamulila atiunikila mmene zinthu zilili ku Germany, Kum’mawa kwa Africa, na ku Bahamas. Ationetsanso mmene abale na alongo athu akupangila Yehova kukhala pothaŵilapo pawo.