NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA June 2024

Magazini ino ili na nkhani zophunzila mu mlungu wa August 12–​September 8, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 23

Ciitano Capadela ca Yehova Cokhala Alendo Ake

Yophunzila mu mlungu wa August 12-18, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 24

Khalani Mlendo m’Tenti ya Yehova Kwamuyaya!

Yophunzila mu mlungu wa August 19-25, 2024.

MBILI YANGA

Yehova Anamva Mapemphelo Anga

N’ciyani cinapangitsa M’bale Marcel Gillet ali mwana kukhala wotsimikiza kuti Yehova ni “Wakumva pemphelo”?

Mafunso Ocokela kwa Oŵelenga

N’cifukwa ciyani ena amaganiza kuti mawu akuti “mudzawayang’anila” a pa Salimo 12:7 amanena za “Mawu a Yehova” ochulidwa mu vesi 6, pomwe Baibulo la Dziko Latsopano limaonetsa kuti mawuwa akunena za anthu “ovutika” ochulidwa mu vesi 5?

NKHANI YOPHUNZILA 25

Muzikumbukila Kuti Yehova ni “Mulungu Wamoyo”

Yophunzila mu mlungu wa August 26–​September 1, 2024.

NKHANI YOPHUNZILA 26

Pangani Yehova Kukhala Thanthwe Lanu

Yophunzila mu mlungu wa September 2-8, 2024.