Onani zimene zilipo

Yakobo—Munthu Amene Anali Kukonda Mtendele

Onani zinthu zambili zimene Yakobo anacita kuti akhazikitse mtendele. Mfundo zake zacokela pa Genesis 26:12-24; 27:41–28:5; 29:16-29; 31:36-55; 32:13-20; 33:1-11.

Mungakondenso Izi

MAPHUNZILO AMENE TINGATENGEMO M’BAIBO

Yakobo Analandila Coloŵa

Isaki na Rabeka pamodzi na ana awo aŵili amphundu. Maina awo anali Esau na Yakobo. Popeza Esau ndiye anali woyamba kubadwa, anali kudzalandila coloŵa capadela. N’cifukwa ciani anasinthanitsa coloŵaco na mbale imodzi ya cakudya?

MAPHUNZILO AMENE TINGATENGEMO M’BAIBO

Yakobo na Esau Akhalanso pa Mtendele

N’cifukwa ciani Yakobo anadalitsidwa na mngelo? Nanga anacita ciani kuti akhalenso pa mtendele na Esau?